Redemption in Christ international Ministries - Zomba Branch

  • Home
  • Malawi
  • Zomba
  • Redemption in Christ international Ministries - Zomba Branch

Redemption in Christ international Ministries - Zomba Branch Redemption in Christ Zomba branch is led by evangelist Mike Williams a son of prophet Leman.

11/10/2025
11/10/2025

Ambuye akudalisen mulibwanji
Tisaiwale kupemphelela malawi

11/09/2025

Ambuye akudalisen mulibwanji

28/07/2025

Njila imodzi yakuchita bwino pamoyo wauzimu ndiko kupemphela kosaona nyengo

16/07/2025
11/06/2025

Samalani ndi ena amene mumacheza nawo ena alipenepo kuranda ndalisowako
Kuranda banjalako kuchinga sogololako
Komanso kuonongabiliyako anthu enawa tisamare nawo ambuye akudalisen mulungu akupasen chokhumba chanu

Mulungu akupasen ntendere wamuntima kwa inu amene mukusowa ntendere Mulungu apeleke machiliso kwa amene mukusowa machili...
09/06/2025

Mulungu akupasen ntendere wamuntima kwa inu amene mukusowa ntendere
Mulungu apeleke machiliso kwa amene mukusowa machiliso
Mulungu apeleke banja Kwa amene mukusowa banja
Mulungu apeleke ntchito kwa amene mukusowa ntchito
Ambuye akudalisen yendani ndi yesu

Address

Malosa
Zomba

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Redemption in Christ international Ministries - Zomba Branch posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share