GOD NEVER FAIL

GOD NEVER FAIL Is only God who is having the final say in your life, trust Him🙏

I am a primary teacher, but I choose to spread the gospel of Jesus... I am Evangelist in the house God🙏 to God be the glory.

27/08/2024

"I shall not die, but live and declare the works of the Lord "
Psalms 118:17
Pempheran pokaniza mzimu wa imfa pa moyo wanu 🙏

21/05/2024

KODI MOYO NDI CHIYANI ??
------- ----------- ---------
Ngati mukufuna ku mvesa bwino kuti Moyo ndi Chani ?
Pitani Mmalo Atatu awa ;.
_____
1.KU CHIPATALA
2.KU NDENDE
3.KU MANDA .
______
1.KU CHIPATALA:- Muzamvesa kuti Palibe chinthu chopambana kuposa ku khala ndi Moyo wa
thanzi wosadwala dwala. Anzathu zipatalamu akuvutika, akunva ululu kuposa kugona ndi njala.
2.KU NDENDE:- Muzamvesa kuti kuchita zinthu mwa Ufulu uli kunja kuno Ndi chinthu cha mtengo wapatali.

3.KU MANDA muzazindikila kuti; Moyo tili nawowu Siwowunyadira kweni kweni .Chifukwa Dothi tipondayi tsiku lina lizatikwilira .

bwino ndi ichi ; Tinabwela opanda kanthu.
Tizapitanso opanda kanthu .
TIYENI tikhale okhutisidwa ndi Wothokoza Nthawi zonse pa Zomwe Mulungu amatichitila. Mot ngt iweyo ukutha kuwerenga postyi ndiwe odala. Ena ndi Akhungu sawona iweyo lemekeza Mulungu chifukwa ulibe ulumali pa Thupi lako.

Amen

21/05/2024

Kusabeleka kwa Sarah, vuto sanali Sarah.
Kusabeleka kwa Hannah, Vuto sanali Hannah.
Kusabeleka kwa Elizabeti, vuto sanali Elizabeti.
Satana anawona kuti m'mimba mwa Sarah simuli munthu wamba (Isaki).
Satana anawona kuti m'mimba mwa Hannah simuli munthu wamba (Samuel).
Satana anawona kuti m'mimba mwa Elizabeti simuli munthu wamba (Yohane M'batizi).
Nyengo zanu zomwe zikulimbazo vuto si inuyo. Satana wawona chomwe mwanyamula. Satana wawona chimene chingatuluke mwa inu akangolora kuti nyengo zimenezo mudutse. Mwatenga chimdalitso chachikulu inu chomwe chikhonza kudzetsa chisokonezo kumidima, nchifukwa chake Satana akulimbitsa nyengo zimenezo. Koma nkhani yabwino ndi yakuti Satana ndi olephera. Pitilizani kumukhulupilira Ambuye ndipo nanu muzakhala ndi umboni ngati Sarah, Hannah komanso Elizabeti.

04/05/2024

Umati ndalephera koma utayamba, osaziyang'anira pansi, Mulungu Alinanu
MUSAOPE🙏

22/03/2024

Anthu amangodziwa kuweruza moyo wako pa zomwe akuona paiwe, koma Mulungu amadziwa zomwe ukudutsamo ndi chifukwa chomwe ukudutsira muzimenezo, ndipo amapeleka njira yothana ndi zovuta zonsezo. I declare long life upon you in Jesus mighty name, ndikutsusana ndi mzimu waimfa pamoyo wako, ozimangilira kapena kumwa poison chifukwa chamavuto, Ambuye akupulumutse mu mthunzi waifa umenewu, Hallelujah!!!!🙏

12/10/2023

I declare, today God will favour your life with uncountable miracles
In Jesus name!!!!

Address

Zomba

Telephone

+265990233183

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when GOD NEVER FAIL posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share