Kaphirintiwa ccap youth

Kaphirintiwa ccap youth Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Kaphirintiwa ccap youth, Religious organisation, Salima.

14/01/2026

Tiyeni tizikhala bwino ndi anthu mu mchaka chimenechi

15/09/2025

Tsiku lija ndi Mawa
Tiyeni tikavote mosamala motsogozedwa ndi ambuye.
Komanso we should pray kuti chisankho chiyende bwino.

27/08/2025

Tsiku lija ndi Mawa lomwe Msonkhano timawudikira uja wafika kuja Ku mpatsa. Uwutu ndi msonkhano opatsa chikoka kwambiri chifukwa tikakamba za makwaya Ali komweku, ndakatulo, Mpunga, masewero, nyama, mpira, mzimu oyera, mamasulidwe, kuguba, ma soulmate Ali komwekuso . Ndiye wina mkumati akhala? Chibwana et? Odi ndizilongeza katundu Wanga ine mukandipeza. Osayiwala kutenga uniform, nyimbo, bible chofunda, zovala zosithira, beseni, card ♦️, soap, mbale , cup, spoon, mafuta ndi ndalama yodyera. Tikuti kumpatsa kukayaka MotoπŸ”₯πŸ”₯πŸ”₯, sizomazandifusa kuti kunali zotani, sizanena.

Happy wedding anniversary Abusa ndi  Mayi Busa Kambiri
03/08/2025

Happy wedding anniversary Abusa ndi Mayi Busa Kambiri

24/07/2025

IFE A EXECUTIVE

tikulengeza za msonkhano motere,
MALO; Kaphirintiwa p\h
TSIKU; pa 26 loweluka

thaw ndi mmawa zafiken mutakozeka paja kuli chimphwando chainu okonda kuimba makwaya,


KWA ZONE YOMWE SIDAPELEKE NDALAMA ZA MSONKHAN PA 26 MUDZAFUSIDWA KU VESTELE THAWI YATHA,

Happy birthday Rev.Alexander Kambiri Timakunyadirani Abusa pitirizani ntchito yabwino yomwe mukugwira.
19/07/2025

Happy birthday Rev.Alexander Kambiri Timakunyadirani Abusa pitirizani ntchito yabwino yomwe mukugwira.

19/07/2025

Happy birthday Rev.Alexander Kambiri. Timakunyadirani Abusa pitirizani ntchito yabwino yomwe mukugwira.

It's a special day to our friends in Christ, Aubrey Z. ChiombagutaHappy birthday mzathu wa youth, let's join him to cele...
13/07/2025

It's a special day to our friends in Christ, Aubrey Z. Chiombaguta
Happy birthday mzathu wa youth, let's join him to celebrate his birthday here we go πŸ₯³πŸ₯³πŸŽŠ

Happy birthday Chisomo Yenga, mzathu wa youth, let's join him to celebrate his birthday, here we go πŸ₯³πŸ₯³πŸ₯³
09/07/2025

Happy birthday Chisomo Yenga, mzathu wa youth, let's join him to celebrate his birthday, here we go πŸ₯³πŸ₯³πŸ₯³

Happy birthday Getu, mzathu wa youth uyu.Lets join her to celebrate her birthday πŸŽ‚πŸŽ‚
08/07/2025

Happy birthday Getu, mzathu wa youth uyu.
Lets join her to celebrate her birthday πŸŽ‚πŸŽ‚

07/07/2025

Happy birthday Mayi odziwika bwino from masintha ccap. Yang'anayang'ana mmmhu

Address

Salima

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Kaphirintiwa ccap youth posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share