Chimbiri CCAP Nkhoma Synod

Chimbiri CCAP Nkhoma Synod Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Chimbiri CCAP Nkhoma Synod, Full Gospel Church, Ntchisi.

16/08/2026

Mawu alero achoka pa

1 Yohane 1 vs 5 mpaka 8

KUYENDA MU KUWUNIKA

15/06/2026

Mulungu amatikonda tose ndipo tiyen tizimuyamika nthaw zose pakut ena sanadzuke ndi moyo koma ife watikondera tiyen tizinena zikom

Ndi m'mene kuliri ku Chimbir CCAP
24/05/2026

Ndi m'mene kuliri ku Chimbir CCAP

24/05/2026

Tili live pa Chimbir CCAP pamwambo womasula Rev . K Maenje

24/05/2026

Mwadzuka bwanj abale ndi alongo kulikose muli Lero nditsiku la chimwemwe kuno ku Chimbir CCAP pomwe kuli mwambo wawukulu womasula abusa Rev. K. Maenje amene akhala akutumikra pa mpingo uno wa Chimbir CCAP kwa zaka zokwana zinayi (4).

Abusa Maenje akupita ku Kasungu kumpingo wa Chitau CCAP, iwowa akumasulidwa lero pa 24 may 2026 ndipo akalandilidwa pa 31 may 2026 ku mpingo wa Chitau.

mwambo wose uli motereeee
malo: Chimbir CCAP Church
Nthawi: 8:00am

Kukakhala azathu wolalika mukuyimba monga, Chimbir chigwirizano choir, Kawenda Miseza Salvation, Nandeta Chigwirizano choir ndi ena ambiri.

Mulungu akutsogoreren pamene muybekeza kudzakhala nawo pa mwambo wawukulu wumenewu amen.
C.C.A.P Nkhoma Synod.

21/05/2026

Mwadzuka bwanj abale ndi alongo mwachimwemwe tilikukuyitanani ku mwambo womasula a busa Rev. K. Maenje.

Rev. K Maenje amene amatumikira pa mpingo wa Chimbir CCAP Church tsopano akupita kukatumikira ku Kasungu ku mpingo wa Chitau CCAP.

Mwambo wose uli motereeee:::
Malo: Chimbir CCAP Church
Nthawi : 8:00am
Tsiku : Lamungu pa 24 May 2026

Aliyese ali wolandilidwa kumwambo umenewu ndipo Mulungu akutsogoreren pamene muybekeza kudzakhala nawo pa mwambo umenewu

Wosayiwala upanga Follow page lanthuli la

CCAP Nkhoma Synod

Address

Ntchisi

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Chimbiri CCAP Nkhoma Synod posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share