Zion prophecy church of god in malawi

Zion prophecy church of god in malawi Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Zion prophecy church of god in malawi, Religious organisation, Mchengautuwa xol, Mzuzu.

kodi mutayenda lero ndichani chodabwina mwakumana nacho chomwe ndichachikulu kwainu?1,moyo waulele.2,banja losangalasa.3...
24/03/2026

kodi mutayenda lero ndichani chodabwina mwakumana nacho chomwe ndichachikulu kwainu?

1,moyo waulele.
2,banja losangalasa.
3,ndalama.
timve nawo chosangalasa chanu

24/03/2026

mulungu wathu ndi wamoyo inuyo wakuzusani bwanji?
ngati simukumva bwino mthupi osadandaula ndi njila yomwe iye anapanga kuti muzaduse,pompano mukhala bwino.

23/03/2026

HOT LIN 0997740267

chose mufuna ku nkhani ya mavuto amu uzimu ndi mthupi muwapeza
ambuye akuyendeleni usiku uno.

muli ndi ufulu wosankha yesu kapena satana,wanu ndi uti:1 yesu Christu...........2 satan mudyelekezi...posankha muwona m...
23/03/2026

muli ndi ufulu wosankha yesu kapena satana,wanu ndi uti:

1 yesu Christu...........

2 satan mudyelekezi...

posankha muwona momwe mukuchitira mayendedwe anu akuuzani komwe mwasankha.

23/03/2026

ngati wina sakumva bwino mthupi mazulo ano ndipemphere naye mzina la yesu.

23/03/2026

kusala ndi kwabwino kumatiyanjanisa ndi yesu christu takhala mwezi tikusala tamasula zana ku edingen mboma la mzimba.

22/03/2026

mwa yesu muli chitemwa nakuzaya

18/03/2026

mzimu wa mulundu ukasika umapanga zomwe walamulidwa,
David analamulidwa kukapha mwana wake mumozi yekhayo ndipo anasatira.
kuvinaso umachita kulamulidwa ndi mzimu woyera

moyo wa mwa yesu kukoma inu
12/03/2026

moyo wa mwa yesu kukoma inu

Address

Mchengautuwa Xol
Mzuzu

Opening Hours

Monday 09:00 - 12:00
Wednesday 04:00 - 06:00
Friday 09:00 - 06:00
Sunday 09:00 - 12:00

Telephone

+265881825881

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Zion prophecy church of god in malawi posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share