Thuchila Living Waters Church

Thuchila Living Waters Church THE HOME OF GRACE The year of harvesting bondfully

Zopembezera za Lero pa 4 January 2026 ( Day 3 of prayer and fasting)PEMPHERO LOPEMPHELERA UTSOGOLERI WA MPINGO (AHEBRI 1...
04/01/2026

Zopembezera za Lero pa 4 January 2026 ( Day 3 of prayer and fasting)

PEMPHERO LOPEMPHELERA UTSOGOLERI WA MPINGO (AHEBRI 13 v 7)

- Adalitseni Atumwi Dr. S.S Ndovie ndi banja lawo lonse

- Pempherani kuti Mulungu awalimbikitse achiwiri awo, Atumwi Dr. B. Chapo ndi nzeru

- Mulungu awapatse Mphamvu ma Bishop, ma Reverend komanso Abusa wonse kuphatikizapo Atsogoleri wonse kulikonse kumene ali

- Tikuwapempherera Atsogoleri wonse kuti chisomo chichulukire pamoyo wawo

Zopembezera za lero pa 3 January 2026, lomwe lili tsiku la chiwiri la kusala kudya. (2/30 days)
03/01/2026

Zopembezera za lero pa 3 January 2026, lomwe lili tsiku la chiwiri la kusala kudya. (2/30 days)

Address

Mulanje
Mulanje

Opening Hours

Monday 07:30 - 17:00
Tuesday 07:30 - 17:00
Wednesday 07:30 - 17:00
Thursday 07:30 - 17:00
Friday 07:30 - 17:00
Saturday 09:00 - 12:00
Sunday 08:30 - 21:00

Telephone

+265995230218

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Thuchila Living Waters Church posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share