Bethsaida Madzi Amoyo Ministry - Utumiki

Bethsaida Madzi Amoyo Ministry - Utumiki Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Bethsaida Madzi Amoyo Ministry - Utumiki, Religious organisation, Milambo Village, Blantyre, Mpemba.

01/06/2026

*ZOTSATIRA ZA KUSANKHA YEHOVA KUKHALA LINGA LAKO πŸ™πŸ½πŸ™πŸ½πŸ™πŸ½πŸ’ͺ🏼πŸ’ͺ🏼πŸ’ͺπŸΌπŸ‘πŸ½πŸ‘πŸ½πŸ‘πŸ½*
Masalimo : 91 : 2-9. Ndidzanena za Yehova, β€œIye ndiye pothawira panga ndi linga langa, Mulungu wanga amene ndimadalira.” 7. Anthu 1,000 atha kufa pambali pako, anthu 10,000 kudzanja lako lamanja, koma zoopsazo sizidzafika pafupi ndi iwe.9. Pakuti wasankha Wammwambamwamba kukhala malo ako okhalamo; wavomera Yehova kukhala kothawira kwako.
*Hallelujah πŸ™πŸ½πŸ™πŸ½πŸ‘πŸ½πŸ‘πŸ½!!Nthaw zonse anthufe timavutika,kuphedwa kuzuzika kmaso nyengo zowawa osatha cifukwa ca cisankho cathu,Nthaw ina ake mukaona kt anthu amene amalimbana ndi Davide ambiri a iwo amakhulupirira ziwanda kapena kt mafano,and muona kt anthu onsewa akafika pamaso pa Davide amagonjetsedwa,Davide amapambana nkhondo zambiri cifukwa anaika Mulungu patsogolo ndikudalira Iye nthaw zonse,Ndipo Davide waona mitundu ambiri a anthu akufa ku nkhondo,Ena mbali iyi,enaso mbali inayi kmaso nkhondo irionse amapambana,Izi cinali chifukwa cosankha Yehova kukhala pasogolo pake πŸ™πŸ½πŸ™πŸ½πŸ™πŸ½πŸ‘πŸ½πŸ‘πŸ½πŸ‘πŸ½πŸ™ŒπŸ½πŸ™ŒπŸ½πŸ™ŒπŸ½*

27/12/2025

οΏ½οΏ½οΏ½Za Ambuye iziοΏ½οΏ½οΏ½οΏ½

24/12/2025

Gogo Nasineya, Grace Bandesi founder of Bethsaida Madzi Amoyo Ministries

Address

Milambo Village, Blantyre
Mpemba

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Bethsaida Madzi Amoyo Ministry - Utumiki posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share