Called by Grace Tv

Called by Grace Tv Called to spread
Faith | Grace | Truth & survation
(1)

Good morning brethren
18/08/2026

Good morning brethren

17/08/2026

Celebrating my 2nd year on Facebook. Thank you for your continuing support. I could never have made it without you. 🙏🤗🎉

14/08/2026

Osalola adaniwo k*t afeee
Akuyenela k*t awone chipambano chako

Chioma Okafor adakana kusewelera team ya Malawi ya Scorchers posankha Nigeria ngakhale adabadwira ku Malawi. Chioma yemw...
14/08/2026

Chioma Okafor adakana kusewelera team ya Malawi ya Scorchers posankha Nigeria ngakhale adabadwira ku Malawi.

Chioma yemwe mayi ake ndi Patricia Jia Okafor a ku Ntcheu komaso bambo ake a m'dziko la Nigeria adapanga chisankho chosewelera dziko la Nigeria mwina chifukwa choti Nigeria ili ndi mbiri yotenga zikho zochuluka kuposa ma scorchers.

Lero zinthu zija zatembenuka, mwala wokanidwa uja wasanduka wa pa ngodya, ma scorchers apeza mwayi wokasewela ku World cup pomwe Nigeria ilibe chiyembekezo chenicheni.

Kodi kunena k*ti kumaliopa mawa mkulakwa?
All in all congratulations to Malawi

11/08/2026

Join my page the3see what we are busy for

Let's move togetherLook at me i try my best but monetization is avoiding me
09/08/2026

Let's move together
Look at me i try my best but monetization is avoiding me

Business timeFocus on your duty
02/08/2026

Business time
Focus on your duty

Umu ndi momwe Bingu National Stadium ikuonekera m'mawa uno, patatha phwando la nyimbo lomwe linachitika dzulo.Mneneri wa...
02/08/2026

Umu ndi momwe Bingu National Stadium ikuonekera m'mawa uno, patatha phwando la nyimbo lomwe linachitika dzulo.

Mneneri wa Unduna wa Zamasewero, Macmillan Mwale, anati udzu sunawonongeke chifukwa panayalidwa chitetezo pa bwalolo.

(Wolemba ndne B Called by Grace Tv)

02/08/2026

Support my small company please contact 0994412744 Bascos

31/07/2026

Wapanga izi ndaniii

Address

Mangochi

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Called by Grace Tv posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share