CHAWA CCAP Nkhoma SYNOD

CHAWA CCAP Nkhoma SYNOD CHAWA CCAP NKHOMA SYNOD is a religious organization with the aim of spreading the Gospel (Good News) throughout the world.

08/08/2026
07/08/2026

Mphunzi presbytery msokhano wa pa Chaka.

Tikupatsirani phunziro lachiwiri mu tsiku la msokhano wayamba dzuro.

MUTU WA MSOKHANO
THAMANGANI KUTI MUKALINDIRE. 1 akorinto 9 vs 24.

02/08/2026

APOLOGIES/ KUPEPESA

Tikupepesa kwa onse omwe mumatsatira mapemphero athu kuti lero talephera kukupatsirani mapemphero a lero pa 2nd August, 2026 pa page yathu ino. izi zachitika chifukwa cha zovuta zina. tikupepesa chifukwa cha izi

05/07/2026

ULALIKI WA PA 5 JULY, 2026

MUTU: KUKHALA PA MASO PA MULUNGU

BUKU : 1 SAMUELI 9 VS 1 - 5

MFUNDO ZIKULUZIKULU

1. Akhristu ambili timakhala mu mpingo koma osamudziwa Yesu ndipo imeneyi ndi ngozi

2. Tikadzuka ndi moyo tidzichitenga chisomo kuti tidzibwerera pamaso pa Mulungu kukagonja pa zosaenera zomwe timachita

3. Kubwerera pa maso pa Mulungu kudzatipatsa chipulumutso komaso chisomo chokalandila korona wa moyo

03/07/2026

CHIDZIWITSO

Mawa, loweluka, pa 4th June, 2026. Ambuye akalola tionetsa live service ya kumangochi, Monkeybay CCAP komwe Praise team yathu yapita kukacheza ndi anzathu ku mpingo wa Monkeybay CCAP.

Address

BOX 2
Lobi

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when CHAWA CCAP Nkhoma SYNOD posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share