15/06/2026
Achinyamata kutsanzikana ndi abusa komaso mayi busa v.k Dyson pa 14 June 2026
Achinyamata taphunzira zambiri kudzera mwa abusawa tasithika ndi utumuki umene Mulungu anapereke kwa Iwo kuti udzafikire youth pa mpingo WA demera tidzawakumbukirabe mpaka kale.