Taymiyah TV

09/07/2026

🎓 🎓

Ndi chisangalalo chachikulu tikukuitanirani kuti mudzakhale nafe pa mwambo wa Graduation JALSAH, tsiku lodzadzidwa ndi chimwemwe, kuyamika Allah, ndi kukondwerera zipatso za khama ndi kupilira komwe Ana ophunzira Anali nako mu nyengo yawo yosaka maphunziro.

Kupezeka kwanu kudzawonjezera ulemerero ndi chisangalalo pa tsiku lapaderali. Bwerani mudzagawane nafe mphindi zosaiwalika pamene tikukondwerera gawo latsopano la moyo.

Musaphonye! Tikuyembekezera kubwera kwanu ndipo mudzakhala olandiridwa.
Taymiyah TV

Sikuti mwayi uliwonse umene ukufuna ndi umene wakonzedwa kuti ukhale wako. Nthawi zina umayesetsa kwambiri munthu, koma ...
03/07/2026

Sikuti mwayi uliwonse umene ukufuna ndi umene wakonzedwa kuti ukhale wako. Nthawi zina umayesetsa kwambiri munthu, koma zinthu osamayendabe. Izi sizimatanthauza kuti ndiwe munthu okanika kapena wolephera ayi. Zimangotanthauzirat kuti njira imeneyoyo siinali yabwino kwa iwe komanso si nthawi yake yomwe Allah analemba kuti makomo ako azabwino atseguke .

🪶🪶🪶🤌

1. Osaamakakamira zinthu zimene zikukana.
2. Kuvomereza kuti pali mwayi wina wabwino umene ukukuyembekezera.
3. Kupitiriza kuyesetsa, koma kukhala oleza mtima ndi kukhulupirira kuti nthawi yoyenera ikafika, chitseko choyenera chidzatseguka.

WOPEREKA🤌🪶
02/07/2026

WOPEREKA🤌🪶

🪶Taymiyah TVစာတို
01/07/2026

🪶
Taymiyah TV
စာတို

29/06/2026

📢 UTHENGA WAPADERA KWA ACHINYAMATA CHISILAMU.

Assalāmu 'Alaikum wa Raḥmatullāhi wa Barakātuh.

Tikukuyitanirani achinyamata nonse a Chisilamu a m'madera oyandikira kaliyeka 1 (Area 21) kuti tiyeni tikhale limodzi mu gulu lachisilamu la achinyamata (Islamic Youth Group) yathu, yotchedwa "RISING UMMAH"

Cholinga chathu ndi kulimbikitsana pa chipembedzo, kuphunzira Qur'an ndi Sunnah, kuwonjezera maphunziro a Chisilamu, komanso kulimbikitsana pa makhalidwe abwino ndi ubale wabwino pakati pa achinyamata.

Bwerani mudzakhale mbali ya gulu lomwe likulimbikitsa kumvera Allah ndi kutsatira Sunnah ya Mtumiki ﷺ.

mukufuna kudziwa zambiri, imbani foni kwa oyang'anira a gululi.👇🏾👇🏾

+265995956113

Allah atiike pa choonadi ndi kutipatsa kupambana. Āmīn.
စာတို Taymiyah TV

          🪶
26/06/2026

🪶

25/06/2026


, 🪶KULIMBA MTIMA
16/06/2026

, 🪶
KULIMBA MTIMA

Address

Area 21
Lilongwe
100

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Taymiyah TV posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share