Central Malawi Conference Adventist Youth Ministries

Central Malawi Conference Adventist Youth Ministries Adventist Massages to all the world in my Generation.

12/08/2026

Atolankhani kuno. Kwachemelatu kuno ma church kulibe kumvutikanso pano

KUTSEGULIRA KWA MISASA YA ACHINYAMATAPa 10  August,2026,  Mtsogoleri wa achinyamata mchigawo cha pakati mu Mpingo wa Sev...
12/08/2026

KUTSEGULIRA KWA MISASA YA ACHINYAMATA

Pa 10 August,2026, Mtsogoleri wa achinyamata mchigawo cha pakati mu Mpingo wa Seventh-day a Busa a Solomoni Naliya anatsegulira misasa ya Achinyamata amchigawowa omwe adzamalize pa 16 August,2026.

Poyankhula ndi a Naliya kutsegulira misasayi anati mkumanowu ndiofunikira kwambiri popeza kukhala kuphuzira zosiyanasiyana zopidula miyoyo

Linda Thandaza

Ngodzi Camp Site Media

12/08/2026

MAJOWAJOWA AM'MADZI

Kuno ku Ngodzi m'boma la Salima m'dziko lino la Malawi,Achinyamata a Mpingo wa Seventh-day akuchita msonkhano wawao wa misasa mmbali mwanyanja.

Achinyamata wa anabwera kuno pa 9 August,2026 ndipo akuyembekezeka kudzamaliza maphunziro awo pa 16 August, 2026.

Kupatula maphunziro,achinyamatawa akumakhala ndi majowajowa omwe omwe akumachitikira mmadzi pomwe akumaphunzira ukadulo osambira mmnyanja.

Poyankhula ndi Boston Chapata yemwe ali mphumzitsi wa kusambira panyanja, wati ndikofunika zedi kuphuzitsa achinyamata mmene angasamambilire panyanja

Nothando Lijenda

Ngodzi Camp Site Media

FLAG RAISING CEREMONYDuring the on going CMC Youth Camps which started from 9th August, 2026 and is scheduled to end on ...
12/08/2026

FLAG RAISING CEREMONY

During the on going CMC Youth Camps which started from 9th August, 2026 and is scheduled to end on 16th August, 2026, today on 12/08/2026, there was flag raising ceremony.

Leading the ceremony were Pathfinders from Salima who did it beautifully.

Flags raised were of Senior Youth, Pathfinder and Malawi National flag

According to Master Guide Master Banda, who is CMC Vice Drill and Uniform Coordinator, the flag raising ceremony is for identity of Adventist Youths, he added that the flags will lowered before the sunset

Different Anthems were subg during the ceremony ie Adventist Youth Umbrella Anthem, Pathfinder Anthem and Malawi National Anthem.

Gracious Kaunda

Area 24 SDA Church

Ngodzi Camp Site Media

MAPHUNZIRO AKUPITILIRA KU MISASA YA A ACHINYAMATA Achinyamata omwe asonkhana kuno ku Ngodzi ku Salima komwe kuchitika mi...
12/08/2026

MAPHUNZIRO AKUPITILIRA KU MISASA YA A ACHINYAMATA

Achinyamata omwe asonkhana kuno ku Ngodzi ku Salima komwe kuchitika misasa ya achinyamata amchigawo Cha pakati omwe anayambika pa 9 August ndipo ndipo amaliza pa 16 August, 2026 akuphunzira maphunziro osiyanasiyana.

Ena mwa maphunzirowa ndi kulemba nkhani zokhudza mpingo ndikuzitumza mmasamba a Mchezo osiyasiyama omwe akupangitsa ndi Victor Mangwalala owe ali mkulo ofalitsa nkhani za achinyamata Mmalawi muno.

Poyankhula ndi a Mangwalala, anati maphunziro akuyenda bwino ndipo achinyamata atswirika ndipo tsopano ndi akadaulo polemba ndikutumiza nkhani.

Blessings Mkuwatha

Ngodzi Camp Site Media

ENCOURAGED TO ENTREPRENEURSAs CMC Youth Camps are currently underway at Ngodzi in Salima,which was officially opened on ...
12/08/2026

ENCOURAGED TO ENTREPRENEURS

As CMC Youth Camps are currently underway at Ngodzi in Salima,which was officially opened on 10th August, 2026 by CMC Youth Director Pastor Solomon Naliya ,Youths has been encouraged to be entrepreneurs.

"You should be involved in small business" Said Naliya

Speaking with Central Malawi Conferenc AYM Vice Education Coordinator, Jeremiah Mpasu, confirmed that about 500 Pathfinders and Senior Youths are attending the camps

The gathering is also blessed with the presence of Pastor Macford Malingaliro who is the Camp Counselor and Pastor Peter Chibwato who is the Camp Pastor while Pastor Solomon Naliya is the Camp Director.

Lonjezo Clements Thumba (Nkhotakota Central Church)
Ngodzi Camp Site Media

12/08/2026

Izizi ndi za daily, zimafunika kunkhala ndi Mphamvu. Enanu simudakakwanitsa🤣🤣🤣

11/08/2026

Crafts and honors inside CMC youth camp.

11/08/2026

Ku Area 47 SDA church media ipita mtsogolo tsopanotu. Adah awawa Ali serious mu camp.

Address

Central
Lilongwe
CMCAYM

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Central Malawi Conference Adventist Youth Ministries posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share