26/04/2026
Inu ku church kunali bwa?
Chipembedzo Cha lero chinalalikidwa ndi Elder Gundasi pa mutu "kod ungadziwe bwanji k*t wapulumutsidwa?"
Inali thaw yopambana kwambiri tsiku la lero ....anawerenga ma bukhu angapo mongs
Genesis 2 vs7-9, yohane 7:38 ndi 39