Mtengo Wa Moyo

Mtengo Wa Moyo The only way to heaven is JESUS CHRIST.

No other church is recommended in the Bible other than Church of Christ
17/11/2024

No other church is recommended in the Bible other than Church of Christ

01/11/2024

Ngat mwadzuka ndi Moyo thank God πŸ™πŸ™πŸ™
Ambiri amafuna atatero km zavuta

29/09/2024

Wokondedwa ngat mumamukonda ambuye apangeni invite anthu ena KT nawonso uthenga wa Ambuye usamawasemphe πŸ™πŸ™πŸ™

18/09/2024

Don't forget to praise the lord πŸ™πŸ™

13/09/2024

My beloved brothers and sisters don't allow the power of Devil to use ur life.Dont forget devil will only use u and leaving u suffering he is killer run away.
May God be with you all the time Amen πŸ™πŸ™πŸ™

12/09/2024

The Lord is good all the time find ur time and read

AGALATIYA 5:15

11/09/2024

[Yohane: 3:36
Aliyense wokhulupirira Mwanayo ali ndi moyo wosatha, koma iye amene samvera Mwanayo sadzawuona moyo, pakuti mkwiyo wa Mulungu umakhala pa iye.”]

10/09/2024

Abale ndi alongo tiyeni tiwerenge 1 YOHANE 2:1-3
Pali mawu omwe Mulungu watikozera amenπŸ™

09/09/2024

Ambiri mwaife timayembekeza KT Mulungu adzachita kutipeza ndkumachita machimo anthuwo km mawu a Mulungu sali chomwecho pakt MATEYU 7:6_7 mawu a Mulungu akt tigogode KT atitsekulire kupanda kutero tidzafa auchimo

08/09/2024

Abale Kms alongo tiyeni tiwerenge 1 akorinto 6:9-10 tisanagone ambuye akhale nanu

MATEYU 3 : 2nanena, Tembenukani mitima; chifukwa Ufumu wa Kumwamba wayandikira.
08/09/2024

MATEYU 3 : 2

nanena, Tembenukani mitima; chifukwa Ufumu wa Kumwamba wayandikira.

Address

Lilongwe

Telephone

+265998921381

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Mtengo Wa Moyo posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Place Of Worship

Send a message to Mtengo Wa Moyo:

Share