Salvation Faith Youth Team - The Amapiano Choir

Salvation Faith Youth Team - The Amapiano Choir The Amapiano Choir

Join the ministry
Gospel | Word | Youth Vibes | Purpose
0996153388 bookings
(4)

Patatha masabata 4 nyimbo yathu ya   Yomwe tinaimba ndi Debbie N yakhala ili mu top 20 pa MBC Radio 2 ndipo week ino Til...
15/06/2026

Patatha masabata 4 nyimbo yathu ya Yomwe tinaimba ndi Debbie N yakhala ili mu top 20 pa MBC Radio 2 ndipo week ino Tili #6 kuchokera pa #8 sabata yatha.

Zikomo kwambiri Ambuye mukuchita zazikulu komaso mwapadera tikuthokoza nonse omvera komaso inu omwe mumaisankha nyimboyi.

Link ili mu comment section muionere bwinobwino.

14/06/2026
Happy birthday Mentor Alex Nkalo.
12/06/2026

Happy birthday Mentor Alex Nkalo.

Good luck pamene mwayamba mayeso lero a Standard 8, Ambuye akutsogolere Esinter Makande.
08/06/2026

Good luck pamene mwayamba mayeso lero a Standard 8, Ambuye akutsogolere Esinter Makande.

Tsopano    Yomwe tinaimba ndi Debbie N yakhala mu Top 20 ku Radio Fm kwa Mwezi tsopano ikulira, ndipo pano ili pa   #8 k...
08/06/2026

Tsopano Yomwe tinaimba ndi Debbie N yakhala mu Top 20 ku Radio Fm kwa Mwezi tsopano ikulira, ndipo pano ili pa #8 kuchoka pa #11 sabaya yathayi.

Ife tikusowa kuthokoza pa support yanu, nonse amene mumamvera komaso kusankha nyimbo yathu, Ambuye apitilize kukudalitsani.

Sarah Lackson Banda Mulungu apitilize kukukumbutsa zonse zomwe unakonzekera nthawi ya class komaso zomwe ukumawelenga ku...
08/06/2026

Sarah Lackson Banda Mulungu apitilize kukukumbutsa zonse zomwe unakonzekera nthawi ya class komaso zomwe ukumawelenga kuti usamaiwale ukakhala mchipinda cholemberamo mayeso.

Mwana wakwathu form 2 Mwamaliza kale kwangotsala 2 days basi💐💐💐

Pamene mukhale mukuyamba mayesoa standard 8 lero,  Mulungu akukumbutseni zonse zomwe mumawelenga komaso kuphunzira, kuti...
08/06/2026

Pamene mukhale mukuyamba mayesoa standard 8 lero, Mulungu akukumbutseni zonse zomwe mumawelenga komaso kuphunzira, kuti mayeso muchite bwino .

Mulungu akutsogolere pamene ukuyamba mayeso a Standard 8 lero
08/06/2026

Mulungu akutsogolere pamene ukuyamba mayeso a Standard 8 lero

Wishing you a wonderful birthday filled with joy, good health, peace, and God's abundant blessings. May this new year of...
07/06/2026

Wishing you a wonderful birthday filled with joy, good health, peace, and God's abundant blessings. May this new year of your life bring success, happiness, and the fulfillment of your dreams. Enjoy your special day and have a fantastic year ahead

Address

Area 24
Lilongwe

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Salvation Faith Youth Team - The Amapiano Choir posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share