Altar of worship the Lord

Altar of worship the Lord In God we trust

11/07/2024

Ndikweza maso anga kwa Inu,
kwa Inu amene mumakhala kumwamba.
Taonani, monga momwe maso a akapolo amayangʼana mʼdzanja la mbuye wawo,
monga momwenso maso a mdzakazi amayangʼana mʼdzanja la dona wake,
choncho maso athu ali kwa Yehova Mulungu wathu,
mpaka atichitire chifundo.
Mutichitire chifundo, Inu Yehova mutichitire chifundo,
pakuti tapirira chitonzo chachikulu.
Ife tapirira mnyozo wambiri kuchokera kwa anthu odzikuza,
chitonzo chachikulu kuchokera kwa anthu onyada.
Masalimo 123:1-4

10/07/2024

God is about to change your story. Kaya muli pa zero remember he makes a way where seems to be no way let's comment amen then I will pray for you. Shalom.

Send a message to learn more

22/06/2024

Ndikweza maso anga ku mapiri;
kodi thandizo langa limachokera kuti?
Thandizo langa limachokera kwa Yehova,
wolenga kumwamba ndi dziko lapansi.
Sadzalola kuti phazi lako literereke;
Iye amene amakusunga sadzawodzera.
Masalimo 121:1-3

20/06/2024

Mulungu asitha nyengo zanu si lero kapena mawa ayi koma ilipo thawi yoikika poti samachedwa kapena kufulumira. Chofunika tiyeni tipemphere komanso tidzigwira ntchito molimbika chifukwa ngati sitipemphera ndi kugwira ntchito. Tidzalandila bwanji zithu zimenezi ziziyendera limodzi.

15/06/2024

Mulungu amachita zithu mu thawi yake ndiye osadera khawa ayi chofunika ndi kulimbika ku pemphera.

14/06/2024

Mulungu ali nawe cholinga m'bale wanga ngakhale nyengo zako zikuoneka zolimba koma osayiwala kupemphera thawi zonse poti yakho la mvuto lako ndi Mulungu.

01/06/2024

Mulungu amakonda aliyense ochimwa ndi ndi olugama ndichifukwa inu ndi ine lero lino tili ndi moyo. Ndiye tiyeni tisaiwale kupemphera. Usiku umenewu satana ali ndi ma plan ake ofuna kuononga moyo wanu ndiye timupemphe Mulungu kuti akhale mulonda wathu mu usiku umenewu.

30/05/2024

Mukufuna kulandira dalitso kuchokera kwa Mulungu koma zintchito zanu zosalongosoka pa maso pa Mulungu.

Poti anthu masiku yano mwakonda kunamizidwa koma kukuuzani choona mukudana nazo.

Ndipo ngati simusitha makhalidwe anu oyipa pa maso pa Mulungu, ndithudi mungubudizika ndi mapemphero koma osalandira dalitso. Ndipo mukufa ndi njala chifukwa cha kusala kufuna dalitso koma mitima yanu mwaumitsa osafuna kukhululukira azanu ndi kusiya zoipa.

Lapani lero ndi kuyamba kutumikira Mulungu mu nchoonadi.

29/05/2024

Mwina ndikutheka mwasala kudya, mapiri nde mwakwera, kupemphera tsiku ndi tsiku koma nyengo zanu zosasitha.

Izi zimachitika ndithu, ngati thawi yako sinakwane yoti Mulungu akudalitse koma sizifunika kusiya kusala kudya, kupemphera chifukwa simukudziwa kuti Mulungu akuyakhani mapemphero anu liti. No matter how tough is your situation one day God will answer your prayers.

Thawi zina timakhala mvuto ndifeyo. Mkutheka kupemphera inde timapemphera koma tili ndi zintchito zoipa zomwe timazichita sitimafuna kuzisiya. Sometimes we need to look up on ourselves. Maybe we are the problem.

TSIKU LABWINO

Address

Lilongwe

Telephone

+27661607295

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Altar of worship the Lord posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share

Category