International Christian Assembly Lilongwe, Malawi

International Christian Assembly Lilongwe, Malawi Bringing you Proverbs from the BIBLE that will Transfom your Spiritual and Earthly Life.

That's that
03/09/2016

That's that

This how we as Christians can control  .
02/09/2016

This how we as Christians can control .

30/06/2016

Pepani posakupatsirani uthenga wa ya last week.
Ok. Mutu wa nkhani unali oti: KUPANGA CHUMA. BY: DR ENSON LWESYA.
Nkhani inali yakuti, palibe munthu yemwe ali osaukitsitsa padziko lapasi pano. Chomwe tiyenera kudziwa ndichakuti, Mulungu anapeleka kwa aliyese kuthekela kokhala ndi chuma.
(1)Ena tinapatsidwa maluso osiyanasiyana. Imeneyo ndi mbewu yomwe Mulungu anatipatsa kuti tiyigwilitse ntchito pakupanga chuma pamiyoyo yathu.
(2)Ena chifukwa cha ntchito zomwe timagwira, timadznenera tikha kuti sitingachite bwino chifukwa choti tikugwira ntchito zomwe zimaoneka kuti ndizonyozeka kwa ena. Komwe dziwani kuti, chomwe mukuchipeza kuchokela muntchito yonyozeka yomweyo ndichomwe Mulungu amagwiritsa ntchito pakutukula Miyoyo yathu.
(3)Ena mpaka timafika pomati aaah, bola ndinakabadwila banja ilo sibwezi ndili osauka poti banjalo ndilolemela. Enaso timati mmmmh, bola ndinakabadwila ku America(kumatchula mayiko olemela). Ayi nkhani sikubadwila banja lolemela kapena dziko lolemela. Chimwe chikufunika ndikuzindikila mbeu yomwe Mulungu anaika mwainu. Mukaidzala mbeu imeneyo yembekezela kukolola mosakaika konse. Mau a Mulungu akuti, Dzanja lomwe lifesa zochuluka, zochulukaso ludzatuta, ndipo lomwe lifesa zochepa, zochpaso lidzatuta. Zingoonetseratu kuti Mulungu anaika mbeu m'dzanja la wina aliyese, kwatsala kwa ife kuti tiyifese mbeu imeneyi ndikukolola. Ndipo ngati tifuna kukundika zochuluka tiyeneraso tifese mbeu imeneyi muchuluka. MULUNGU AKHALE NANU.

31/05/2016

Oooh yeah, chapel yalero imakamba za .
Zisankho zimene tingapange lero, ndizomwe zingapangitse lathu kuti likhale labwino kapena ayi. Ngati tasankha kusaphunzira ndiye kuti tisadzadabwe kuti wabwera bwanji.
Ngati tasankha kusagwira ntchito, osadzadabwa kuti mavutowo abwera bwanji.
Let's make right descissions to make our .

28/05/2016

Proverbs 1 verse 5: A wise MAN will hear and increase learning, And a man of understanding will attain wise counsel.. Take heed o this message...

09/01/2016

International Christian Assembly!!!! 2016's theme says is: (ACELERATION) But those who wait on the Lord shall renew their strength; they shall mount up wings like eagles, they shall run and not be weary, they shall walk and not faint. (Isaiah 40 verse 31) I hope we will acelerate.

02/11/2015

It's ICA IMPACT CONFERENCE 2015. From 4th to 8th November. The Host will be; Rev Dr Enson Lwesya & the main speaker is Rev Johannes Mazibuko from Swaziland(Alliance Church).........From Wednesday to Friday, there will be a REVIVAL SESSIONS........Saturday there will be IMPACT LEADERSHIP SEMINAR........And on Sunday there will be ONE JOINT SERVICE from 9AM.
All these are under the THEME: "THE FAMILY THAT IMPACTS GENERATIONS"
VENUE: ICA MARQUEE
WE ARE URGING YOU ALL TO COME AND EXPERIENCE THE PRESENCE AND POWER OF GOD. INTERNATIONAL CHRISTIAN ASSEMBLY, BRINGING PEOPLE OF ALL NATIONS TO CHRIST!!!!!!!!!

Address

Lilongwe
INTERNATIONALCHRISTIANASSEMBLYP.O.BOX1220LILONGWE,

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when International Christian Assembly Lilongwe, Malawi posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share