01/12/2025
I met two boys and one girl, m'malo mowalalikira zam'Bible I just shared with them the facts of this generation...
1 - Amajambulitsa akudya kuma Lodge, alindimbale yampunga. Then ku inbox azikuuza, 'Tigaireni 2pin tigule ndiwo Njala anzanu'.
2 - Amakhala ndima phone odula, koma nkumavutitsa anthu awagulire Bundle.
3 - Background yawo a kuchokera ku pathetic family, koma pano akufuna kumavala zovala za high class, and mafuta odzola ama mk50,000
4 - Saopa matenda, Saopa mimba. Bola adye, a ale, apange zoti wina wake zimuwawe
5 - Busy kukonza thupi, m'malo mokoza Khalidwe
6 - Alibe patience, koma ma shortcuts basi
7 - Nthawi yodzala alibe, koma amafuna kukolora.
8 - Kuwadzudzula saamva, amakukwiira, kukublocker. They don't allow someone to to tamper with their free-world
9 - Za Mulungu ndiye akhala nazo serious. Koma akagwa m'mavuto ndiye kuthamangira kwa anthu opemphera kuti awapemphelere mavuto athe.
10 - They use Pretence as weapon. Pamaso pa anthu kumasekelera, koma kuseri akulira. Ma heart breaks sinkhani.
11 - Amadziwa kusunga zinsinsi, koma sangasunge banja.
12 - Amaonjezera mphamvu zakuchipinda, koma osadziwa kudziletsa.
13 - Amalimbikitsana mtima kuti munthu asamanyengelere munthu, chonsecho iwowo amangopepesa kumbali.
14 - Mijedo nthawi zonse, koma kulephera kukambirana ma business ideas
15 - Wina akalakwitsa, amafuna potchukira
16 - Every move amaiika pa social media
17 - Kudziwa kusunga ma pics ndima videos, koma kulephera kupanga ma savings ku Bank
18 - Online 24/7 kufuna kupeza mnyamata/mtsikana ophweka for s*x and survival
19 - Kumangovula, koma akufuna kumalandira ulemu. Kuiwala kuti ma insects amalondora sweet amene salimpepala
20 - Anyamata mvetserani izi : Chikuni chakhuni cham'mbali mwansewu, osachitengera kunyumba. Anthu amachilondola nkumakachiwazira kunyumba kwanu konko. Ichichi chinazolowera nkhwangwa zosiyanasiyana
21 - Opemphera pa social media, ma verse mkati, koma zinsisi zako nzoopsya.. Tizingoyamika poti Police sinazizindikire zinsisi.
22 - Kugula ma ipods, kumaloweza nyimbo, koma kulephera kugula hard copy Bible
By Blessings Kadam'manja