Vocation Promotion - Archdiocese of Lilongwe

Vocation Promotion - Archdiocese of Lilongwe This page is created to promote vocations to Priesthood and Religious Life within the Archdiocese.

Tiyeni tiwapempherere ma Brother anayi a Chipani cha Marist amene ali pa mbindikiro wao wa masiku 30 okonzekera malumbir...
05/08/2026

Tiyeni tiwapempherere ma Brother anayi a Chipani cha Marist amene ali pa mbindikiro wao wa masiku 30 okonzekera malumbiro awo omaliza.

Akupangitsa mbindikirowu ndi Fr. John Kaliwamba.

Achinyamata mukafuna u brother ndipezeni tilankhulane ngati abale!

Ofesi yowona za maitanidwe mu Archdiocese ya Lilongwe mogwilizana ndi ofesi yowona za achinyamata lero pamene Youth Rall...
29/07/2026

Ofesi yowona za maitanidwe mu Archdiocese ya Lilongwe mogwilizana ndi ofesi yowona za achinyamata lero pamene Youth Rally kuno ku Chayamba Secondary School ili mkati anali ndi mwayi owafotokozera achinyamatawa za maitanidwe osiyasiyana mu mpingo.

Achinyamata kwakoma ndi kuno!

Atsikana mayitanidwe awoooooo
25/07/2026

Atsikana mayitanidwe awoooooo

Atsikana mwayitu uwuuu opita ku usisitere!
24/07/2026

Atsikana mwayitu uwuuu opita ku usisitere!

18/07/2026

Tikuti kunakoma!

18/07/2026

Kwakoma ndikuno

TIWADZIWE A DEACON ATHUDeacon Nathan Banda, a Chipani Cha Capuchin Franciscans ( OFM.Cap) amachokera ku St. John Paul II...
18/07/2026

TIWADZIWE A DEACON ATHU

Deacon Nathan Banda, a Chipani Cha Capuchin Franciscans ( OFM.Cap) amachokera ku St. John Paul II church, Chindande, (Ludzi) Parish. Anabadwa m'banja la ana asanu ndi atatu; atsikana asanu ndi anyamata atatu ndipo iwo omaliza pobadwa.

Maphunziro a Primary anamphunzira sukuku ya Chidzibwe, Chindande Mchinji. Pomwe Secondary anaphunzira pa Magawa, Secondary School, Kamwendo Mchinji.

Anayamba ulendo wao wochita maphunziro a unsembe pa 13 February 2016, ku St.Francis Formation House, Ntcheu,Dedza Diocese.

Kenaka mu mchaka cha 2017 anakapitiliza maphunzilowa ku Zambia , Camerino Novitiate House, komanso ku St. Bonaventure University kwa zaka zitatu maphunziro a Philosophy. Pambuyo pake anakamaliza maphunziro awo a Theology ku Tangaza University Nairobi Kenya, kuchoka Chaka Cha 2021-2025.

Mawu owatsogolera ndi akuti " Sindinu munandisankha koma ndine ndinakusakha" (Yohane 15:16)

The mass is about to start
18/07/2026

The mass is about to start

Zikuterooooo!
18/07/2026

Zikuterooooo!

Address

Lilongwe Archdiocese, P. O. Box 631
Lilongwe

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Vocation Promotion - Archdiocese of Lilongwe posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share