Nkhani zasangulutso

Nkhani zasangulutso Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Nkhani zasangulutso, Religious organisation, Yanjanani, Kwataine.
(1)

21/08/2020

Koma makolo Anu munawauza kuti kwanu ndikwa Merica zoti ndinu student waku charco pa Facebook akuzidziwa kapena simufuna zoyambana ndi munthu ndili pa selipa🏃🏃

31/05/2020

Chibwezi changa chinakaba ndrama kwa Bambo ake,ine ndayambila business ndramayo moti pano zikundiyendera, koma akuti ndimukwatile eti ndizoona ndikwatile mbavayo maganizo anu thandizeni guys

30/05/2020

Pali Sam iyi Koma asala yake ikhre letter,,
1_1=[ ]

27/05/2020

Ndikuzizilaku ndafusa kuti apa ndikumatani Ndaona adona anga akulowa kuchipinda ndye ndikubwera kundiuza kuti tipite kuchipinda ine kuwafusa kuti tikatani akuti tibakathamanga,,ine Sha😋kuthamanga amathamanga opanda ulendo zopusa basi

Address

Yanjanani
Kwataine
134212

Telephone

0630070142

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Nkhani zasangulutso posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share