13/12/2023
let's be in the shoes ya anthu omwe anamwalira they're in Hades waiting for a judgement day....
Do you know that those guys amafunitsitsa atangopasidwa 1 minute kubwera padziko la pansi adzalape ,
Inuyo you're alive koma mukungochimwa , kuyenda ndi azibambo, kusokoneza mabanja a eni zibwezi Zambiri mbiri, kupusisa anthu in the name of prophet yet you're fake, kuminula
You think you're alive k*t inuyo ndi opambana? Or it's normal k*t basi muyenera kukhala moyo? Have you ever asked yourself why you're still alive??
Mulungu akukupasani mwai k*ti mwina muzindikira mulape,koma akangoti enough basitu kwanu kwantha?
One thing you have to know,every second yadutsa umakhala wachosera nthawi yako yokhala padziko lapansi, apapa mukuchotsera nthawi yanu
Enanu mumwalira simulowa chaka chamawa apa,enanu mumwalira next year koma simukuziwa you're there busy uchimo
Anzanu Ali nchipatala uko kuphupha ndi imfa kufuna atamuziwa yesu before Kumwalira and you're there playing with lives ...
Repent , repent ,repent kumanda kulibe kulapa,once wasiya kupuma basi.....Acts:2.38
Peter replied, "Repent and be baptized, every one of you, in the name of Jesus Christ for the forgiveness of your sins. And you will receive the gift of the Holy Spirit.