28/06/2026
Mwambo operekeza m'bale wathu Leo Maulana yemwe anali wapampando wa Choir ya St. Lawrence imodzi mwa ma choir apa St. Mary's Chemusa Catholic Parish ku Blantyre.
Iwowa amachokera m'boma la Balaka.