07/08/2026
بسم الله الرحمن الرحيم
🌿 PANEL DISCUSSION PROGRAM 🌿
Mukuitanidwa mwaulemu ku msonkhano wapadera wa Panel Discussion wokambirana nkhani yofunika kwambiri yokhudza moyo wa banja la Chisilamu polumikizitsa ndi 'Aqīdah." .
📅 Tsiku: Lamulungu, 09 August 2026 CE
📍 Malo: Malambusya, Ulongwe – Balaka
🕣 Nthawi: 08:30 AM – 03:00 PM
🕌 Mutu wa Msonkhano:
"Banja Mchisilamu polumikidzitsa ndi 'Aqīdah."
🎙️ Oyankhula:
• Sh. Twāhā Idrīs Yāsīn
• Sh. Bilāl Ayyām Bwanausi
• Sh. Abū Hashma Hamdān Banda
👥 Oitanidwa: Amuna ndi Akazi, Anyamata ndi Atsikana – aliyense ndi wolandiridwa.
🍽️ Chidziwitso: Chakudya cha masana chidzaperekedwa, In Shā Allāh ﷻ.
Itanani anzanu ndi achibale anu. Tiyeni tikaphunzire limodzi zomwe zingalimbikitse 'Aqīdah yathu ndi kumanga banja lolimba la Chisilamu. Musaphonye mwayiwu wophunzira, kufunsa mafunso, ndi kupindula ndi malangizo ochokera kwa ma Shaykh athu.
Tifalitseni uthengawu kuti nawonso ena azathe kupindula nawo uthenga omwe ukaperekedwa ku panel discussion imeneyi. Barakallāhu fīkum.