15/08/2026
Madzulo abwino kwa nonse.
Uthenga wangotipeza madzuli ano:
Program ya Maliro a Late Mrs Chaponda mwambo wa mpingo udzachitikira mu Church.
Nde kuti Tizayamba ndi Normal service yomwe ikuzayamba 07:00am -09:00am
Kukhomo Kwa chaponda mwambo uzayamba 10:00am ndizoyakhula kenako azanyamula kubwela Ku church.
Tiyeni tiwaziwiseko amzathu.