Ndirande Central S.D.A Church

Ndirande Central S.D.A Church This is a vibrant community of S.D.A believers in Malawi. We exist to share the love of Jesus, the desire of all ages.

You are all invited
14/05/2026

You are all invited

Ifetu ku Ndirande Central tili okondwa chifukwa cha kusankhidwa kwa wathuwathu MG Thom Maiden kukhala wapampando wa utum...
25/04/2026

Ifetu ku Ndirande Central tili okondwa chifukwa cha kusankhidwa kwa wathuwathu MG Thom Maiden kukhala wapampando wa utumiki wa achinyamata mu Eastern Malawi Conference.

Congratulations 💯

Tikumane ku FAM EP launch Sunday li
22/04/2026

Tikumane ku FAM EP launch Sunday li

18/04/2026
18/04/2026

Mutu wa Ulaliki:
Kulimbana Mkati Mwanga

05/04/2026

Tsiku la lero ndilomwe kukuyambika Youth Week of Prayer mu Ndirande 2 district. Msonkhanowu uzichitikira pa Ndirande Central p***a ndipo lero Sunday uyamba nthawi ya 4 Koloko madzulo.

Tiyeni tipezeke ku msonkhanowu.

Otumikira ku msonkhanowu ndi pastor Dr. Luwani

28/03/2026

Live now

Divine Service

Address

Post Office Box 60285
Blantyre

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Ndirande Central S.D.A Church posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share