06/12/2024
Kodi mukudwala, nthenda zodziwika/zosadziwika bwino ndipo mwayesayesa ndipo mwalephera???
Kodi mukusowa chisomo Cha ntchito, business zanu sizikuyenda bwino,
Kodi mwayesa kupeleka moyo wanu Kwa Mulungu pomukhulupirira yesu khristu koma zikuvuta kusintha ndi kuyisa zikhalidwe zosakondweretsa Mulungu???
Kodi moyo wanu ndi wophinjika ndi nyengo,zosowa,zaumphawi,zotonzedwa,zokadwa,zosatha kukhulupiriridwa,malire mmoyo,kusowa mabanja,ana,e,t,c
Kodi muli olema ndi otopa polimbana ndi zonsenzi???
Fikani ndithu ku salvation of Jesus Christ ministries, Thamanda la chipulumutso Cha yesu nkhristu,pa chileka roundabout moyang'ana ndi Ather private school kuti mudzakumane Naye YESU NKHRISTU ndikukupantsani mtendere wokhazikika mu dzina lake la mphanvu ndi loyera
Sunday service 8th October 2024 ndi mtumiki wa mulungu Apostle E.E. Chitwanga.nthawi ya 9:30Am
Tonse odwala,TiYENI tikumbukire kutenga ziphaso zathu za kuchipatala pobwera ku church
Ambuye akudalitseni pamene mukupanga chisankho chopezeka pa pathamanda la chipulumutso Cha yesu nkhristu msabata imeneyi🙏