Balaka Central SDA Church

Balaka Central SDA Church We make disciples through Christ-like living, communicating, discipling, teaching, healing, & serving

26/08/2026

Phee nthawi yankhomaliro, kwinaku tikumvera mingoli yokoma

25/08/2026

Luka 17:35 "Kumbukirani mkazi wa Loti"

Mulungu ndiokhoza kubwenzeretsa inde ngakhale mtima osweka, ngati titamudalira Iye ndikumutulira nkhawa zathu zonse
22/08/2026

Mulungu ndiokhoza kubwenzeretsa inde ngakhale mtima osweka, ngati titamudalira Iye ndikumutulira nkhawa zathu zonse

22/08/2026

Ifenso tagwirizana nazo

22/08/2026

Uphungu wabwino a mmene tingadalitsikire posamalira achikulire

22/08/2026

Tikumakhala nawo motani ana omwe sitinabeleke ndifeyo m'makomo mwathumu? Aliyense aziyankhile payekha

22/08/2026

Nkutheka tili ndi khalidwe la ufalisi, mwina wamsembe, Koma tidziwe kuti anthu ena amatidalira ndithu. Tiyeni tikhale monga msamariya wachifundo uja

22/08/2026

Zimachitikaditu izi. Tiyeni tikhale osamala

22/08/2026

Tikhale nawo mtima wachifundo omwe umakhoza kuchiritsa kusweka mtima konse

22/08/2026

Ana ake ali ofanana ndi nyenyezi zam'mwamba

Address

P. O. Box 80
Balaka

Opening Hours

Wednesday 17:00 - 18:00
Friday 17:00 - 18:00
Saturday 08:00 - 18:00
Sunday 02:00 - 16:30

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Balaka Central SDA Church posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share