Makogolo CCAP

Makogolo CCAP Pray to God

24/10/2022

Mulungu sakondwa ndi imfa ya munthu wochimwa koma wochimwayo alape

30/06/2022

PAKUTI ONSE ANACHIMWA NAPEREWERA PA ULEMERELO WA MULUNGU ,ABALE ANZANGA TONSE TACHIMWA NDIPO TAPEREWERA PA YEHOVAYO

22/06/2022

TIKANENA KUTI TILIBE UCHIMO TIZINYENGA TOKHA NDIPO MWA IFE MULIBEMO CHOONADI

12/06/2022

How is your Sunday people of God

14/05/2022

1AKORINTO 15 V33
MUSASOCHERETSEDWE KUGWIRIDZANA NDI ANTHU OIPA NKUMAWONONGA MAKHALIDWE ANU ABWIMO

11/05/2022

AHEBRI 13 V 1
MUSAIWALE KUCHEREZA ALENDO PAKUTI ICHI ENA ANACHEREDZA ANGELO KOMA OSAWADZIWA

08/05/2022

NGAKHALE NDIYENDA MCHIGWA CHA MTHUZI WA IMFA SINDIDZAOPA CHOIPA PAKUTI INU YEHOVA MULI NANE

03/05/2022

MUYAMBE MWATHANGA UFUMU WACHE KENAKO CHINA CHILICHONSE CHIDZAPASIDWA KWA INU

17/04/2022

HAPPY HAPPY EASTER 🤣🤣🤣🤣🤣🤣

16/04/2022

Pakuti iye ananyozedwa chifukwa Cha zolakwa zathu

Address

Bakili Muluzi High Way
Dubai

Telephone

+265992906259

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Makogolo CCAP posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share